Nanga Inu bwanji

1304

由 Malius Phiri 使用 Suno AI

Nanga Inu bwanji
v4

@Malius Phiri

Nanga Inu bwanji
v4

@Malius Phiri

lyrics
Intro
Thindimani Kay
Nanga Inu bwanji



Verse 1
Usiku nitagona
Ninalotaa
thambo lamwamba
Litatsegukaa
mfumu yama fumu
Inatsika kumwamba
Kudzaweluzaa
Khamu LA anthu ochuluka linasonkhana
Kuzalandira fumu yawo
Yamtendele
Ndi khamu ya anjelo
Yoimba malipenga
Ndi azeze. Ndiyesu mwini
Anali nawo patsogolo
Atanyamula buku lake
Lamayina kulongosola zomwe iye anaziwona
Dziko lino
Anthu ochimwa adafuna
Atazemba nalowelera
mugulu lawolungama
Koma sizinatheke yesu anawadziwa
Nawafusa






Chorus
Nanga inu bwanji
Munkazuza ntundu wanuu
Nanga inu bwanji inu
Munadya chuma chasiye
Unali oipa iwe opondeleza osauka
Unali m'busa iwe osocheletsa nkhosa zanga




Verse 2
Usiku wanga kumaloto ndinawona
Mwala imene amisili anaukana
Zowona ndiwomwewo omwe unasanduka wapangodya
Yesu yemwe anthu ena anamunyoza
Namupachika kwapilatoo
Ndinawona ndinawona
Yemweyo
Anali oweluza dziko lino
Mpando wake wachifumu onyezima
Chakumanja kwa dzanja latate ake
Ndithudi ndiyemweyi yo yemweyo azaweluze dziko losee
Anthu ochimwa adzafuna atazembaa
Nalowelera mugulu lawolungamaa
Koma sizizatheka yesu azawadziwa nawafusaa




Chorus
Nanga inu bwa
Munkazuza NTundu wanuu
Nanga Inu bwanji
Munadya chuma chamasiyee
Unali oipa iwe
Opondeleza osaukaa
Unali m'busa iwe
Osocheletsa nkhosa zangaa
音乐风格
Raggae

你可能会喜欢

歌曲的封面Tingwan
v4

由 Clyde Emmancii 使用 Suno AI 创建

歌曲的封面Un solo latido
v4

由 Rafaela Figueroa Gonzales 使用 Suno AI 创建

歌曲的封面Tu Silla Está Puesta
v4

由 Darwin Solórzano 使用 Suno AI 创建

相关播放列表

歌曲的封面Om Namah Shivaya
v4

由 Banita Rawat06 使用 Suno AI 创建

歌曲的封面Szeretném, ha szeretnél
v4

由 Renátó Strausz 使用 Suno AI 创建

歌曲的封面Notte di Fango
v4

由 OMAR DI CAPUA 使用 Suno AI 创建