M'mudzi Mwathu

40

由Chalera 使用Suno AI

M'mudzi Mwathu
v4

@Chalera

M'mudzi Mwathu
v4

@Chalera

lyrics
(chalela)

[Verse 1]
Mama ku msika
Red tomatoes in her tray
Dzuwa so hot
Koma she’s smiling
Says
“Iweyo
udza-khala dokotala”

Tate ku munda
phazi lili-be sapato kuda
Hoe goes down
Akundiwuza
All this farming for me and you

Chorus]
M'ma-wa ku sukulu
Masana ku mudzi
I'm proud
Ine ndili busy
Kuphunzira
Kuseka
Kuimba nyimbo
Ndi aphu-nzitsi kusukulu kwathu
Ndine wamtengo wapamwamba kwambili

M'mawa ku sukulu
Usiku nthano
Grandma akunena pa-mbali pa moto
Moonlight tikuse-wera
Tiziseka tonse
Ndi anthu a-m'mudzi mwathu
My heart is never lonely (My heart is never lonely)

[reggae melody]

[Verse 2]
Usiku pa moto
Folktales fly like fireflies
Gule wamkulu in my dreams
Ancestors dancing in the skies

Anza-nga kusewela
jingo-janga football by the moon
Koma mam'mawa
Bag on my shoulder
Ndikanyaude ku class-room

Chorus]
Chorus]
M'ma-wa ku sukulu
Masana ku mudzi
I'm proud
Ine ndili busy
Kuphunzira
Kuseka
Kuimba nyimbo
Ndi aphu-nzitsi kusukulu kwathu
Ndine wamtengo wapamwamba kwambili

M'mawa ku sukulu
Usiku nthano
Grandma akunena pa-mbali pa moto
Moonlight tikuse-wera
Tiziseka tonse
Ndi anthu a-m'mudzi mwathu
My heart is never lonely (My heart is never lonely)

[Bridge]
Ndikawona Mama’s hands
Ndiwona story
Lines like rivers
Full of glory
Ndikaona Tate’s field
Green and wide
Ndimalumbira
I’ll carry their pride (oh yeah)

Chorus]
M'ma-wa ku sukulu
Masana ku mudzi
I'm proud
Ine ndili busy
Kuphunzira
Kuseka
Kuimba nyimbo
Ndi aphu-nzitsi kusukulu kwathu
Ndine wamtengo wapamwamba kwambili

M'mawa ku sukulu
Usiku nthano
Grandma akunena pa-mbali pa moto
Moonlight tikuse-wera
Tiziseka tonse
Ndi anthu a-m'mudzi mwathu
My heart is never lonely (My heart is never lonely)

[happiness melody]
音樂風格
The guitar performance uses a simple fingerstyle technique with a repetitive folk-style chord progression, The vocal delivery is intimate, raw, and soulful Male Voice, Afrobeat, Slow Reggae Melody,

你可能會喜歡

歌曲的封面neked
v4

由 György Sz 使用 Suno AI 建立

歌曲的封面Andelai
v4

由 Ruan Lima 使用 Suno AI 建立

歌曲的封面Terra Santa
v4

由 Stefano Lombardi 使用 Suno AI 建立

歌曲的封面Michele De Sciscio Miglior Autista
v4

由 Monster Hunter by Gianluca Amoriello 使用 Suno AI 建立

相關播放列表

歌曲的封面козленок и фонарик 3
v5

由 Сергей Троллев 使用 Suno AI 建立

歌曲的封面Countryside Daydream
v4

由 Oleh Po 使用 Suno AI 建立

歌曲的封面OVERDOSE
v4

由 вахаии 使用 Suno AI 建立

歌曲的封面Genesis Flow"
v5

由 Людмила Балаевалапкапавленко 使用 Suno AI 建立