Me

964

由Chifuniro Sofaya 使用Suno AI

Me
v4

@Chifuniro Sofaya

Me
v4

@Chifuniro Sofaya

lyrics
Intro
Eeeey chifu ase


( Verse 1)

Eyiii yanga ija kunja kwacha
Msanadzuke ndi tcheke FB
Ndapeza meseji ya malama
Ati wasowatu ase
Ndati ize osadanda tigwilana pasanaduse mwezi
Kenako dyaku wazahala
Ati ndasowatu wezi ..ine shaa
Apa mzanga wandithawapo koma ati tizakumana buddy

(Chorus)
Ati life ndichoncho ase osamadanda
Koma nanga ndiiwala bwanji friend
Asalawa amakuonesa chikondi chabodza kuseli kumakujeda wezi
Pomwe zibwana timapanga koma mijedo simbali yathu
Poti mwati life ndichoncho
Kwaife tingoti tizagwirana eee


(Verse 2)
Pamene paja ndadandalapo zatha koma zkundivuta kuiwala wezi poti unali dyaku poselewulana paja zokwiyatu simbali yako eeeh
Kenako ndati ndiyendeko ndazakumana nd faifiesi
Basitu yathu ija zibwana tinthabwala mpaka takafika kutali wezi kuima pachiwaya komano cha mbalaga tiwaleko tsabola wezi umakwana umakwana iweyootu umakwana ase eee

(Chorus )
Ati life ndichoncho ase osamadanda
Koma nanga ndiiwala bwanji friend
Asalawa amakuonesa chikondi chabodza kuseli kumakujeda wezi
Pomwe zibwana timapanga koma mijedo simbali yathu
Poti mwati life ndichoncho
Kwaife tingoti tizagwirana eee
音樂風格
Dancehall

你可能會喜歡

歌曲的封面Gps
v4

由 Alberto Martuzzi 使用 Suno AI 建立

歌曲的封面باسم الحق
v4

由 سمير عسكب 使用 Suno AI 建立

歌曲的封面Tam, gdzie tańczy wiatr
v5

由 Jerzyna K 使用 Suno AI 建立

歌曲的封面JESZCZE BLIŻEJ
v5

由 Jerzyna K 使用 Suno AI 建立

相關播放列表

歌曲的封面خايف إني كون بحبك
v4

由 osama abotrapa 使用 Suno AI 建立

歌曲的封面Марго
v4

由 Влада Мирошник 使用 Suno AI 建立

歌曲的封面'86
v4

由 Bence Oravecz 使用 Suno AI 建立

歌曲的封面Zero Hamulców
v5

由 slawomir 使用 Suno AI 建立