SHUT-UP

80

Musik skapad av bryan mphande med Suno AI

Cover av låten SHUT-UP
SHUT-UP
v6 Mini

@bryan mphande

Cover av låten SHUT-UP
SHUT-UP
v6 Mini

@bryan mphande

Text
Iwe vuto yako nibwanji everytime
umakamba problem ya banzanu koma yako
wankhalapo iwe ziiiiii
Everyday umamakhala na tuma group twa boza
manje chakutengela ati wa president nio dwala
uche ba president niodwa ukhala nao
naye nimunthu monga ise tifunika kumupemphelela
ngati adwala pakuti choipa chikabwela
sungakhalepo president iwe

chorus
SHUT-UP YOUR MOUTH
IT MIGHT BE YOU
GOING FASTER THAN
YOU COME OOOOYEEEE

moyo wamunthu aliyense uli mumanja mwa mulungu
ndiye amaziwa nthawi yathu tonse
manje iwe ulibe mphanvu yoziba zamoyo munthu
Iwe vuto yako nibwanji everytime
umakamba problem ya banzanu koma yako
wankhalapo iwe ziiiiii
Everyday umamakhala na tuma group twa boza
manje chakutengela ati wa president nio dwala
uche ba president niodwa ukhala nao
naye nimunthu monga ise tifunika kumupemphelela
ngati adwala pakuti choipa chikabwela
sungakhalepo president iwe
moyo wamunthu aliyense uli mumanja mwa mulungu
ndiye amaziwa nthawi yathu tonse
manje iwe ulibe mphanvu yoziba zamoyo munthu
aliyonse manga kamwa yako
tizaba vamene mufuna sikukamba chabe nikamwa
imakuvutani koma sindimwe mumapasa moyo
so just

chorus
SHUT-UP YOUR MOUTH
IT MIGHT BE YOU
GOING FASTER THAN
YOU COME OOOOYEEEE

Sikwaise kukonkha mendo yanthu mwamene tapita
pakuti oro sisi yanthu sitingaikwase kupenda
Olo ba church kwamanidabwisa mumazonda munthu
palibe chifukwa muchosa vovala koma ndeu siyanu
niye nkhani mumachomelela che
nakamwa siimababapo na vinthu vaboza
wakakugwilani mumadaula
phunzisani kamwa yanu kukamba vabwino
so ine nikamba kuti

chorus
SHUT-UP YOUR MOUTH
IT MIGHT BE YOU
GOING FASTER THAN
YOU COME OOOOYEEE
Iwe vuto yako nibwanji everytime umakamba problem ya banzanu koma yako wankhalapo iwe ziiiiii Everyday umamakhala na tuma group twa boza manje chakutengela ati wa president nio dwala uche ba president niodwa ukhala nao naye nimunthu monga ise tifunika kumupemphelela ngati adwala pakuti choipa chikabwela sungakhalepo president iwe chorus SHUT-UP YOUR MOUTH IT MIGHT BE YOU GOING FASTER THAN YOU COME OOOOYEEEE moyo wamunthu aliyense uli mumanja mwa mulungu ndiye amaziwa nthawi yathu tonse manje iwe ulibe mphanvu yoziba zamoyo munthu Iwe vuto yako nibwanji everytime umakamba problem ya banzanu koma yako wankhalapo iwe ziiiiii Everyday umamakhala na tuma group twa boza manje chakutengela ati wa president nio dwala uche ba president niodwa ukhala nao naye nimunthu monga ise tifunika kumupemphelela ngati adwala pakuti choipa chikabwela sungakhalepo president iwe moyo wamunthu aliyense uli mumanja mwa mulungu ndiye amaziwa nthawi yathu tonse manje iwe ulibe mphanvu yoziba zamoyo munthu aliyonse manga kamwa yako tizaba vamene mufuna sikukamba chabe nikamwa imakuvutani koma sindimwe mumapasa moyo so just chorus SHUT-UP YOUR MOUTH IT MIGHT BE YOU GOING FASTER THAN YOU COME OOOOYEEEE Sikwaise kukonkha mendo yanthu mwamene tapita pakuti oro sisi yanthu sitingaikwase kupenda Olo ba church kwamanidabwisa mumazonda munthu palibe chifukwa muchosa vovala koma ndeu siyanu niye nkhani mumachomelela che nakamwa siimababapo na vinthu vaboza wakakugwilani mumadaula phunzisani kamwa yanu kukamba vabwino so ine nikamba kuti chorus SHUT-UP YOUR MOUTH IT MIGHT BE YOU GOING FASTER THAN YOU COME OOOOYEEE
Musikstil
Afro jazz, Kalindula feel, kizomba, drum roles in bridges, bass guitar, lead guitar, keyboard, 85-116

Du kanske gillar

Relaterad spellista

Cover av låten WRACAM DO SIEBIE
v4

Skapad av Jerzyna K med Suno AI

Cover av låten Shadow no Fim
v4.5

Skapad av Djan Lima Souza med Suno AI

Cover av låten Kocham Cie
v4.5

Skapad av Wojciech “Boyka” Witczak med Suno AI

Cover av låten Everybody Knows the Move
v4

Skapad av Daruta Vera med Suno AI