Iwe vuto yako nibwanji everytime umakamba problem ya banzanu koma yako wankhalapo iwe ziiiiii Everyday umamakhala na tuma group twa boza manje chakutengela ati wa president nio dwala uche ba president niodwa ukhala nao naye nimunthu monga ise tifunika kumupemphelela ngati adwala pakuti choipa chikabwela sungakhalepo president iwe
chorus SHUT-UP YOUR MOUTH IT MIGHT BE YOU GOING FASTER THAN YOU COME OOOOYEEEE
moyo wamunthu aliyense uli mumanja mwa mulungu ndiye amaziwa nthawi yathu tonse manje iwe ulibe mphanvu yoziba zamoyo munthu Iwe vuto yako nibwanji everytime umakamba problem ya banzanu koma yako wankhalapo iwe ziiiiii Everyday umamakhala na tuma group twa boza manje chakutengela ati wa president nio dwala uche ba president niodwa ukhala nao naye nimunthu monga ise tifunika kumupemphelela ngati adwala pakuti choipa chikabwela sungakhalepo president iwe moyo wamunthu aliyense uli mumanja mwa mulungu ndiye amaziwa nthawi yathu tonse manje iwe ulibe mphanvu yoziba zamoyo munthu aliyonse manga kamwa yako tizaba vamene mufuna sikukamba chabe nikamwa imakuvutani koma sindimwe mumapasa moyo so just
chorus SHUT-UP YOUR MOUTH IT MIGHT BE YOU GOING FASTER THAN YOU COME OOOOYEEEE
Sikwaise kukonkha mendo yanthu mwamene tapita pakuti oro sisi yanthu sitingaikwase kupenda Olo ba church kwamanidabwisa mumazonda munthu palibe chifukwa muchosa vovala koma ndeu siyanu niye nkhani mumachomelela che nakamwa siimababapo na vinthu vaboza wakakugwilani mumadaula phunzisani kamwa yanu kukamba vabwino so ine nikamba kuti
chorus SHUT-UP YOUR MOUTH IT MIGHT BE YOU GOING FASTER THAN YOU COME OOOOYEEE
Iwe vuto yako nibwanji everytime umakamba problem ya banzanu koma yako wankhalapo iwe ziiiiii Everyday umamakhala na tuma group twa boza manje chakutengela ati wa president nio dwala uche ba president niodwa ukhala nao naye nimunthu monga ise tifunika kumupemphelela ngati adwala pakuti choipa chikabwela sungakhalepo president iwe chorus SHUT-UP YOUR MOUTH IT MIGHT BE YOU GOING FASTER THAN YOU COME OOOOYEEEE moyo wamunthu aliyense uli mumanja mwa mulungu ndiye amaziwa nthawi yathu tonse manje iwe ulibe mphanvu yoziba zamoyo munthu Iwe vuto yako nibwanji everytime umakamba problem ya banzanu koma yako wankhalapo iwe ziiiiii Everyday umamakhala na tuma group twa boza manje chakutengela ati wa president nio dwala uche ba president niodwa ukhala nao naye nimunthu monga ise tifunika kumupemphelela ngati adwala pakuti choipa chikabwela sungakhalepo president iwe moyo wamunthu aliyense uli mumanja mwa mulungu ndiye amaziwa nthawi yathu tonse manje iwe ulibe mphanvu yoziba zamoyo munthu aliyonse manga kamwa yako tizaba vamene mufuna sikukamba chabe nikamwa imakuvutani koma sindimwe mumapasa moyo so just chorus SHUT-UP YOUR MOUTH IT MIGHT BE YOU GOING FASTER THAN YOU COME OOOOYEEEE Sikwaise kukonkha mendo yanthu mwamene tapita pakuti oro sisi yanthu sitingaikwase kupenda Olo ba church kwamanidabwisa mumazonda munthu palibe chifukwa muchosa vovala koma ndeu siyanu niye nkhani mumachomelela che nakamwa siimababapo na vinthu vaboza wakakugwilani mumadaula phunzisani kamwa yanu kukamba vabwino so ine nikamba kuti chorus SHUT-UP YOUR MOUTH IT MIGHT BE YOU GOING FASTER THAN YOU COME OOOOYEEE
النمط من الموسيقى
Afro jazz, Kalindula feel, kizomba, drum roles in bridges, bass guitar, lead guitar, keyboard, 85-116