Ndimitima yokodwera

1299

Music Created By Thomzy maganizo With Suno AI

Ndimitima yokodwera
v4

@Thomzy maganizo

Ndimitima yokodwera
v4

@Thomzy maganizo

Lyrics
Ndi mitima yokondwera
Mbuye wathu tiyamika.

E, chifundo chake chonse
Ndichosatha nthawi zonse.

2 Dzina lake tibukitsa,
Mlungu ndiye yekhayekha.

3 Mphamvu yake inalenga
Dziko lonse ndikumwamba

4 Anatsogolera kale
M'chipululu anthu ake.


Ine dzakwera mwamba ndi angero ine ine. dzakwera mwambaaa ine dzakwera mwamba. ndi angero ine dzakwera mwambaaa ine. dzakwera mwambaaa. ndi angero ine dzakwera. mwambaaa.


5 Ndi chifundo atipenya
Ife anthu osauka.

6 Amaweta nyama zonse,
Zingasowe kanthu konse.


7 Tiimbire Mlungu wathu
Waulemu ndi wamkulu

8 Tithawire kwa Mulungu,
Ndiko tikapeze moyo.




Ine dzakwera mwamba ndi angero ine ine. dzakwera mwambaaa ine dzakwera mwamba. ndi angero ine dzakwera mwambaaa ine. dzakwera mwambaaa. ndi angero ine dzakwera. mwambaaa.
Style of Music
Afro bongo

You Might Like

Cover of the song Ma
v4

Created By TheMarcsicica Marcsi With Suno AI

Cover of the song Take on me
v4

Created By Maurizio Morrison With Suno AI

Cover of the song Ajkad édes mint a méz
v4

Created By Balázs Imóhy With Suno AI

Related Playlist

Cover of the song T.N.T
v4

Created By Peter Hellström With Suno AI

Cover of the song Hola
v4

Created By Enzo With Suno AI