Kumaloto
v3.5

@Willard Chirwa

Kumaloto
v3.5

@Willard Chirwa

가사
Intro
Mmmmm!
Ooooo! Yeah
Winzo cee
BLACK LEOPARD EMPIRE
Vip heeeeeeee!!
Verse 1
Kumaloto fanz imatifila
Sound pamalawi kumamangilira
Nyimbo zathu kunvekano pa wayiles
Osatifuna mu ghetto Ali very less
Mabeib ambiri kumangotilora
Tuma superhero kuma controller
Osanamizana ghetto
inatilora
Eve show kumapanga zidola
Osanamizana ifeyo tinatchuka
Black leopard aise inaveka
Chomwe tikufuna chilichose chimatheka
Kumapanga collable aise ndichitheka
Usiku uliwonse kumachenja guys
Chiseko ku empayaso tinakiya
Osanamizana ifeyo tina blower omwe anatuluka akufunaso kulowa
Hook
Kumaloto empire ndiotchuka
Kumaloto empire ndiyonveka
Ndati kumaloto akaz amatilira
Sound pamalawi kumamangilira
Kumaloto empire ndiotchuka
Kumaloto empire ndiyonveka
Ndati kumaloto akaz amatilira
Sound pamalawi kumamangilira
Vers2
Ndudabwa queen beib aise akundihala
Akuti winzo cee tiye ukandpushe show
Pompo tanyamuka kuvaya
L city
Titafika titapeza mafanz ambiri
Ochukuka heavy kuposa aman city
Kushow ndtabwerako pa4n
Kumacheza matext ndi joynathu
Akuti black leopard empire akaypangeno interview
Few hours ndinakhola k binzo
Kut amuuzeko pattern
Kut waku Monday mwezi uno pa 10
Amuuzekoso man d kutulo tikapange zinthuz
Amuuzekoso m star
Hook
Kumaloto empire ndiotchuka
Kumaloto empire ndiyonveka
Ndati kumaloto akaz amatilira
Sound pamalawi kumamangilira
Kumaloto empire ndiotchuka
Kumaloto empire ndiyonveka
Ndati kumaloto akaz amatilira
Sound pamalawi kumamangilira
음악 스타일
Dancehall

당신은 좋아할 수도 있습니다

노래 표지 Балаган

Suno AI을 사용하여 Ев «kapakapa» Ка에 의해 생성됨

노래 표지 A Szitek útja 8

Suno AI을 사용하여 Zoltán Légrádi에 의해 생성됨

노래 표지 Ты воевал и не пришёл домой

Suno AI을 사용하여 Интернет магазин 1INGOLF에 의해 생성됨

노래 표지 Pasja w Dźwiękach

Suno AI을 사용하여 Gronix Games에 의해 생성됨

관련 재생목록

노래 표지 Freedom in the Moonlight

Suno AI을 사용하여 Familjen Hermansson에 의해 생성됨

노래 표지 Te

Suno AI을 사용하여 kicsirob에 의해 생성됨

노래 표지 No jode

Suno AI을 사용하여 Yiro Pérez에 의해 생성됨

노래 표지 Brechas

Suno AI을 사용하여 Rodrigo Pérez에 의해 생성됨