歌詞
Yeah.
Yeah. Madolo amu ghetto yanga. osazapepelesa ndi zomwe amapanga. mukati muonesese anthuwa ndi mashasha.
Maka osatengela ndizomwe amapanga.
(Verse)
Ambili amati muli mafana olowelera zaumbuli akuonena ngati tikusochela. Nde osamadabwa tikamazichemelera. Titukuka bwanji anthu mkutipondeleza, komanso kutikhomelera. Ife ndi mafana opusha osamanyoza mwina poti timasuta nde ndimadana ndizoti uko azindisusa. Yeah Ongah!