Family

469

Nhạc được tạo bởi Lyson Petros bằng Suno AI

Family
v3.5

@Lyson Petros

Family
v3.5

@Lyson Petros

Lời bài hát
Ine Desire ndifotokoze zatsikulanga
Lero kusewu ndayenda ndisamu
Ndipo kusukulu ndimakhozaso Masamu
Agogo anandipatsa ndalama ndipo ndinakagula sikono
Mayi akandituma sindinenaso nono
Ine Patricia lero anandibweza kumadzi,
Nditakatunga ndinachapa zovala koma sopo sindinathire wambiri chifukwa tizovala tinali tiwiri
Madzuro ano ndadyera mazira
Komaso ndkuweruka kumene pa Nsika
Ndatopa ndifuna ndikagone
Kutimwina ndipume ndikalote
Lero ndinapita kuoda
Ndakatenga tomato osaola
Ndinakachezaso ndachina Roda
Mayi Ajuniyo amafuna andibwereke ziwiya ndikaonetse kugulu
Kuti anzanga asakandinene ndikhale mfulu
Ine Layisoni ndimasewera game
Kenako ndinapita kwamadala kukaonera mpira
Pano ndinakula ndinasiya kuphika
Pano tilipo anthu folo mnyumba muno ndipo tose timagwirizana
Nyimboyi ndiya Desire komaso Patricia
Disire, Patricia, Ellina ndi Layisoni ndife Banja limodzi
Phong cách âm nhạc
Raggae

Bạn có thể thích

Danh sách phát liên quan

Bìa bài hát Friend zone
v4

Được tạo bởi Christopher Lombe Với Suno AI

Bìa bài hát Не ходи за мной
v4

Được tạo bởi Oksana Aliohina Với Suno AI

Bìa bài hát Песня ЧФК
v4

Được tạo bởi Nat Po Với Suno AI

Bìa bài hát война разумов
v4

Được tạo bởi Хуторянин Про Với Suno AI