lyrics
[Verse]
Ndikanaziwa kuti unali chochi
Bweza mwina nditaponya voti
Poti iwe unanditaya mdothi
Kundimenya yakumbuyo ngati
[Prechorus]
Mwina ndine gonthi
Aaaa iwee
[Chorus]
Mesa unali ngelo
Paka kumaganiza kuti ndikuvaka velo
I think I'm gonna go
Mesa unali ngelo
[Verse 2]
I think of you I think of the pain
Ndikaganiza za iwe
I feel it again and again
Ndikaganiza za iwe
[Prechorus]
I think I am gonthi
Aaaa iwe
[Chorus]
Mesa unali ngelo
Paka kumaganiza kuti ndikuvaka velo
I think I'm gonna go
Mesa unali ngelo