INTRO Ace Train HOOK Bulijeti ine ndimakukonda aaaa Ndimakufila aaaaa ndimakulota aaaaa Bulijeti ine ndimakukonda aaaa Ndimakufila aaaaa ndimakulota aaaaa VERSE1 Buliget ine ndimakukonda kukuuza zoona ndimakufila ndipo ndikamagona ndimalota iwe ndiwanga wapa mtima panga Sindifuna kuti uzasinthe mawanga ayii cause your my only lover Weyo ndine mati mati Coz your my sinyolita VERSE2 Kukuuza ineyo ndimakukonda olo utapitakukawafusa amakeloda Ndipo ndizakusamala ndizakuchengeta sizakusiya moyo wanga onse cause your my only lover Weyo ndine mati mati Coz your my sinyolita HOOK Bulijeti ine ndimakukonda aaaa Ndimakufila aaaaa ndimakulota aaaaa Bulijeti ine ndimakukonda aaaa Ndimakufila aaaaa ndimakulota aaaaa OUTRO Ace Train JON-LAIH ON THE MIX